Oweruza 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndipo Baraki anasonkhanitsa pamodzi fuko la Zebuloni+ ndi fuko la Nafitali ku Kedesi, moti amuna 10,000 anam’tsatira,+ ndipo Debora nayenso anapita nawo. 1 Samueli 25:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ndiyeno mphatso*+ imene kapolo wanu wamkazi wabweretsa kwa inu mbuyanga, muipereke kwa anyamata amene akutsatira mapazi anu.+
10 Ndipo Baraki anasonkhanitsa pamodzi fuko la Zebuloni+ ndi fuko la Nafitali ku Kedesi, moti amuna 10,000 anam’tsatira,+ ndipo Debora nayenso anapita nawo.
27 Ndiyeno mphatso*+ imene kapolo wanu wamkazi wabweretsa kwa inu mbuyanga, muipereke kwa anyamata amene akutsatira mapazi anu.+