Aheberi 11:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Iwo anali abwino kwambiri, osayenera kukhala m’dziko lotereli. Anayenda uku ndi uku m’zipululu, m’mapiri, m’mapanga,+ ndi m’maenje a dziko lapansi.
38 Iwo anali abwino kwambiri, osayenera kukhala m’dziko lotereli. Anayenda uku ndi uku m’zipululu, m’mapiri, m’mapanga,+ ndi m’maenje a dziko lapansi.