2 Samueli 17:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndipo tsopano tumizani uthenga mwamsanga kwa Davide+ wakuti, ‘Lero musagone m’chipululu, muwoloke ndithu+ kuopera kuti inu mfumu pamodzi ndi anthu onse amene muli nawo mungamezedwe.’”+
16 Ndipo tsopano tumizani uthenga mwamsanga kwa Davide+ wakuti, ‘Lero musagone m’chipululu, muwoloke ndithu+ kuopera kuti inu mfumu pamodzi ndi anthu onse amene muli nawo mungamezedwe.’”+