2 Samueli 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mefiboseti mwana wa Yonatani, mwana wa Sauli, atalowa ndi kuonana ndi Davide, nthawi yomweyo anagwada n’kuwerama mpaka nkhope yake pansi.+ Pamenepo Davide anati: “Mefiboseti!” Poyankha, iye anati: “Ndine pano mtumiki wanu.”
6 Mefiboseti mwana wa Yonatani, mwana wa Sauli, atalowa ndi kuonana ndi Davide, nthawi yomweyo anagwada n’kuwerama mpaka nkhope yake pansi.+ Pamenepo Davide anati: “Mefiboseti!” Poyankha, iye anati: “Ndine pano mtumiki wanu.”