Deuteronomo 25:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Iwo anakumana nanu panjira ndi kupha anthu oyenda movutika m’gulu lanu amene anali kumbuyo. Iwo anachita izi pamene munali olefuka ndi otopa ndipo sanaope Mulungu.+ 2 Samueli 16:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Patapita nthawi, mfumu ndi anthu onse amene anali naye anafika kumene anali kupita ali otopa. Choncho iwo anaima kuti apume.+
18 Iwo anakumana nanu panjira ndi kupha anthu oyenda movutika m’gulu lanu amene anali kumbuyo. Iwo anachita izi pamene munali olefuka ndi otopa ndipo sanaope Mulungu.+
14 Patapita nthawi, mfumu ndi anthu onse amene anali naye anafika kumene anali kupita ali otopa. Choncho iwo anaima kuti apume.+