2 Samueli 19:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Ndiyeno Barizilai+ Mgiliyadi nayenso anatsika kuchokera ku Rogelimu. Iye anapita ku Yorodano pamodzi ndi mfumu. Barizilai anaperekeza mfumu mpaka kukafika ku Yorodano.
31 Ndiyeno Barizilai+ Mgiliyadi nayenso anatsika kuchokera ku Rogelimu. Iye anapita ku Yorodano pamodzi ndi mfumu. Barizilai anaperekeza mfumu mpaka kukafika ku Yorodano.