Ezekieli 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Tenga tirigu,+ balere, nyemba zikuluzikulu,+ mphodza,+ mapira, ndi tirigu wamtundu wina.*+ Zonsezo uziike mumphika umodzi kuti zikhale chakudya chako cha masiku amene udzakhale ukugonera mbali imodzi. Udzadye chakudya chimenechi kwa masiku 390.+
9 “Tenga tirigu,+ balere, nyemba zikuluzikulu,+ mphodza,+ mapira, ndi tirigu wamtundu wina.*+ Zonsezo uziike mumphika umodzi kuti zikhale chakudya chako cha masiku amene udzakhale ukugonera mbali imodzi. Udzadye chakudya chimenechi kwa masiku 390.+