2 Samueli 2:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Tsopano Yowabu analiza lipenga la nyanga ya nkhosa,+ ndipo anthu onse anaima, moti sanapitirizenso kuthamangitsa Isiraeli. Iwo sanayambirenso kumenyana.
28 Tsopano Yowabu analiza lipenga la nyanga ya nkhosa,+ ndipo anthu onse anaima, moti sanapitirizenso kuthamangitsa Isiraeli. Iwo sanayambirenso kumenyana.