2 Mafumu 9:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Mlonda wa pansanja uja ananenanso kuti: “Munthu tamutuma ujanso wakumana nawo, koma sakubwerera. Ndipo mmene anthuwo akuthamangira, akuthamanga ngati Yehu+ mdzukulu wa Nimusi,+ pakuti iye amathamangitsa galeta ngati wamisala.”+
20 Mlonda wa pansanja uja ananenanso kuti: “Munthu tamutuma ujanso wakumana nawo, koma sakubwerera. Ndipo mmene anthuwo akuthamangira, akuthamanga ngati Yehu+ mdzukulu wa Nimusi,+ pakuti iye amathamangitsa galeta ngati wamisala.”+