2 Samueli 18:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndiyeno Ahimazi+ mwana wa Zadoki anati: “Ndiloleni ndithamange ndikapereke uthenga kwa mfumu, chifukwa Yehova wamuweruza kuti amulanditse m’manja mwa adani ake.”+
19 Ndiyeno Ahimazi+ mwana wa Zadoki anati: “Ndiloleni ndithamange ndikapereke uthenga kwa mfumu, chifukwa Yehova wamuweruza kuti amulanditse m’manja mwa adani ake.”+