Miyambo 12:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Maganizo a anthu olungama ndiwo chilungamo.+ Utsogoleri wa anthu oipa ndi wachinyengo.+