Salimo 140:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Anthu amene amakonza chiwembu mumtima mwawo,+Amene amandiukira tsiku lonse ngati mmene zimakhalira pankhondo.+ Miyambo 6:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 mtima wokonzera ena ziwembu,+ mapazi othamangira kukachita zoipa,+ Miyambo 11:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Zolakalaka za anthu olungama, ndithu n’zabwino.+ Chiyembekezo cha oipa chimabweretsa mkwiyo woopsa.+ Yeremiya 4:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tsuka mtima wako ndi kuchotsa zoipa zonse, iwe Yerusalemu, kuti upulumuke.+ Kodi maganizo ako oipawo udzakhala nawo mpaka liti?+ Mateyu 26:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iwo anali kupangana+ zoti agwire Yesu mochenjera ndi kumupha.
2 Anthu amene amakonza chiwembu mumtima mwawo,+Amene amandiukira tsiku lonse ngati mmene zimakhalira pankhondo.+
23 Zolakalaka za anthu olungama, ndithu n’zabwino.+ Chiyembekezo cha oipa chimabweretsa mkwiyo woopsa.+
14 Tsuka mtima wako ndi kuchotsa zoipa zonse, iwe Yerusalemu, kuti upulumuke.+ Kodi maganizo ako oipawo udzakhala nawo mpaka liti?+