Ekisodo 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiyeno Mulungu anati: “Lowetsanso dzanja lako m’malayamo.” Choncho analowetsanso dzanja lake m’malaya. Atalitulutsa anaona kuti lakhalanso bwino ngati poyamba.+ Numeri 12:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pamenepo Mose anayamba kufuulira Yehova kuti: “Chonde Mulungu wanga! M’chiritseni chonde!”+
7 Ndiyeno Mulungu anati: “Lowetsanso dzanja lako m’malayamo.” Choncho analowetsanso dzanja lake m’malaya. Atalitulutsa anaona kuti lakhalanso bwino ngati poyamba.+