1 Mbiri 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mwana wa Solomo anali Rehobowamu.+ Rehobowamu anabereka Abiya,+ Abiya anabereka Asa,+ Asa anabereka Yehosafati,+ Mateyu 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Solomo anabereka Rehobowamu.+Rehobowamu anabereka Abiya.Abiya+ anabereka Asa.+
10 Mwana wa Solomo anali Rehobowamu.+ Rehobowamu anabereka Abiya,+ Abiya anabereka Asa,+ Asa anabereka Yehosafati,+