Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 10:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Kenako Yehu anatumiza uthenga mu Isiraeli+ yense, moti olambira onse a Baala+ anabwera. Palibe ndi mmodzi yemwe amene sanabwere. Iwo analowa m’kachisi wa Baala ndipo kachisiyo anadzaza kuchokera kutsogolo mpaka kumbuyo.

  • 2 Mafumu 10:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Anagwetsanso chipilala chopatulika cha Baala+ ndi kachisi wa Baala,+ ndipo malowo anawasandutsa zimbudzi+ mpaka lero.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena