Ezara 6:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndaikanso lamulo lakuti aliyense wophwanya+ lamulo limeneli, thabwa+ lidzazulidwa panyumba yake ndipo iye adzapachikidwa+ pathabwalo. Komanso nyumba yake idzasandutsidwa chimbudzi cha aliyense chifukwa cha zimenezi.+ Danieli 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mfumuyo inayankha Akasidiwo kuti: “Ine ndikulamula kuti: Amuna inu mukapanda kundiuza malotowo ndi kuwamasulira, mudzadulidwa nthulinthuli+ ndipo nyumba zanu zidzasanduka zimbudzi za anthu onse.+
11 Ndaikanso lamulo lakuti aliyense wophwanya+ lamulo limeneli, thabwa+ lidzazulidwa panyumba yake ndipo iye adzapachikidwa+ pathabwalo. Komanso nyumba yake idzasandutsidwa chimbudzi cha aliyense chifukwa cha zimenezi.+
5 Mfumuyo inayankha Akasidiwo kuti: “Ine ndikulamula kuti: Amuna inu mukapanda kundiuza malotowo ndi kuwamasulira, mudzadulidwa nthulinthuli+ ndipo nyumba zanu zidzasanduka zimbudzi za anthu onse.+