Genesis 40:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Pakapita masiku atatu, Farao akutulutsa n’kukudula mutu. Adzakupachika pamtengo,+ ndipo mbalame zidzadya nyama yako ndithu.”+ Deuteronomo 21:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Pakakhala munthu amene wachita tchimo loyenera chiweruzo choti aphedwe, ndiyeno munthuyo waphedwa,+ ndipo wam’pachika pamtengo,+
19 Pakapita masiku atatu, Farao akutulutsa n’kukudula mutu. Adzakupachika pamtengo,+ ndipo mbalame zidzadya nyama yako ndithu.”+
22 “Pakakhala munthu amene wachita tchimo loyenera chiweruzo choti aphedwe, ndiyeno munthuyo waphedwa,+ ndipo wam’pachika pamtengo,+