1 Mafumu 18:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno Ahabu anauza Obadiya kuti: “Pita m’dzikoli, ukayendere akasupe onse a madzi ndi zigwa* zonse. Mwina tikhoza kupeza udzu wobiriwira+ woti tidyetse mahatchi ndi nyulu, kuti nyamazi zisapitirize kufa.”+ Yobu 6:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ngakhale abale anga amene, achita zachinyengo+ ngati mtsinje woyenda nthawi yozizira,Ngati makwawa a mitsinje yoyenda nthawi yozizira, imene imauma.
5 Ndiyeno Ahabu anauza Obadiya kuti: “Pita m’dzikoli, ukayendere akasupe onse a madzi ndi zigwa* zonse. Mwina tikhoza kupeza udzu wobiriwira+ woti tidyetse mahatchi ndi nyulu, kuti nyamazi zisapitirize kufa.”+
15 Ngakhale abale anga amene, achita zachinyengo+ ngati mtsinje woyenda nthawi yozizira,Ngati makwawa a mitsinje yoyenda nthawi yozizira, imene imauma.