Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 4:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Kenako anapita pabedipo ndipo anagwada n’kuweramira mwanayo.+ Anagunditsa pakamwa pake ndi pakamwa pa mwanayo. Maso ake anakhudzana ndi maso a mwanayo, manja ake anawaika pa manja a mwanayo. Anakhalabe chowerama choncho mpaka thupi la mwanayo linayamba kufunda.

  • Machitidwe 20:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Koma Paulo anatsika pansi, ndipo anadziponya pa iye+ ndi kumukumbatira. Kenako ananena kuti: “Khalani chete, pakuti ali moyo tsopano.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena