Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 2:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Ndiyeno ana a aneneriwo anauza Elisa kuti: “Ife atumiki anu tili ndi amuna 50 amphamvu, bwanji tiwatume kukafunafuna mbuye wanu? Mwina mzimu+ wa Yehova wamunyamula ndipo wam’ponya paphiri linalake kapena m’chigwa.” Koma Elisa anayankha kuti: “Ayi musawatumize.”

  • Ezekieli 3:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Kenako mzimu unanditenga+ ndipo kumbuyo kwanga ndinayamba kumva mawu amphamvu ngati chimkokomo chachikulu,+ akuti: “Utamandike ulemerero wa Yehova kumalo ake.”+

  • Mateyu 4:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Kenako mzimu unatsogolera Yesu kuchipululu+ kuti akayesedwe+ ndi Mdyerekezi.

  • Machitidwe 8:39
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 39 Atatuluka m’madzimo, mzimu wa Yehova unachotsa Filipo mwamsanga pamalopo,+ ndipo nduna ija sinamuonenso, koma inapitiriza ulendo wake ikusangalala.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena