-
2 Samueli 15:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Nthawi yomweyo, Davide anauza atumiki ake onse amene anali naye limodzi mu Yerusalemu, kuti: “Nyamukani, tiyeni tithawe,+ pakuti sipapezeka munthu wopulumuka m’manja mwa Abisalomu. Chitani changu, pakuti mwina angafike mofulumira ndi kutipeza n’kutichitira choipa komanso kukantha mzinda ndi lupanga!”+
-