2 Samueli 17:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Davide anafika ku Mahanaimu+ ndipo Abisalomu nayenso anawoloka Yorodano pamodzi ndi amuna onse a Isiraeli amene anali naye.
24 Davide anafika ku Mahanaimu+ ndipo Abisalomu nayenso anawoloka Yorodano pamodzi ndi amuna onse a Isiraeli amene anali naye.