1 Mbiri 12:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Tsopano nazi ziwerengero za atsogoleri a anthu okonzekera kumenya nkhondo amene anabwera kwa Davide ku Heburoni,+ kudzam’patsa ufumu+ wa Sauli malinga ndi lamulo la Yehova.+
23 Tsopano nazi ziwerengero za atsogoleri a anthu okonzekera kumenya nkhondo amene anabwera kwa Davide ku Heburoni,+ kudzam’patsa ufumu+ wa Sauli malinga ndi lamulo la Yehova.+