2 Samueli 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ku Heburoni analamulira monga mfumu ya Yuda zaka 7 ndi miyezi 6.+ Ku Yerusalemu+ analamulira monga mfumu ya Isiraeli yense ndiponso Yuda zaka 33. 1 Mbiri 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Davide anabereka ana 6 ku Heburoni ndipo analamulira kumeneko zaka 7 ndi miyezi 6. Kenako analamulira zaka 33 ku Yerusalemu.+
5 Ku Heburoni analamulira monga mfumu ya Yuda zaka 7 ndi miyezi 6.+ Ku Yerusalemu+ analamulira monga mfumu ya Isiraeli yense ndiponso Yuda zaka 33.
4 Davide anabereka ana 6 ku Heburoni ndipo analamulira kumeneko zaka 7 ndi miyezi 6. Kenako analamulira zaka 33 ku Yerusalemu.+