Genesis 14:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndipo Melekizedeki,+ mfumu ya ku Salemu,+ anabweretsa mkate ndi vinyo.+ Iyeyu anali wansembe wa Mulungu Wam’mwambamwamba.+
18 Ndipo Melekizedeki,+ mfumu ya ku Salemu,+ anabweretsa mkate ndi vinyo.+ Iyeyu anali wansembe wa Mulungu Wam’mwambamwamba.+