1 Mafumu 15:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Basa atangokhala mfumu, anapha anthu onse a m’nyumba ya Yerobowamu. Sanasiye wa m’banja la Yerobowamu aliyense ali ndi moyo kufikira atawatha onse, malinga ndi mawu a Yehova amene analankhula kudzera mwa mtumiki wake Ahiya Msilo.+
29 Basa atangokhala mfumu, anapha anthu onse a m’nyumba ya Yerobowamu. Sanasiye wa m’banja la Yerobowamu aliyense ali ndi moyo kufikira atawatha onse, malinga ndi mawu a Yehova amene analankhula kudzera mwa mtumiki wake Ahiya Msilo.+