Yoswa 21:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Kuchokera m’fuko la Zebuloni,+ mabanja a ana a Merari,+ amene ndi Alevi otsala, anapatsidwa Yokineamu+ ndi malo ake odyetserako ziweto, Karita ndi malo ake odyetserako ziweto,
34 Kuchokera m’fuko la Zebuloni,+ mabanja a ana a Merari,+ amene ndi Alevi otsala, anapatsidwa Yokineamu+ ndi malo ake odyetserako ziweto, Karita ndi malo ake odyetserako ziweto,