Genesis 1:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Tsopano Mulungu anati: “Dziko lapansi+ likhale ndi zamoyo monga mwa mitundu yake, nyama zoweta,+ nyama zokwawa,*+ komanso nyama zakutchire+ monga mwa mitundu yake.” Ndipo zinaterodi. Miyambo 30:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Mkango, umene ndi wamphamvu kwambiri panyama zonse zakutchire ndiponso umene suopa chilichonse n’kubwerera m’mbuyo,+
24 Tsopano Mulungu anati: “Dziko lapansi+ likhale ndi zamoyo monga mwa mitundu yake, nyama zoweta,+ nyama zokwawa,*+ komanso nyama zakutchire+ monga mwa mitundu yake.” Ndipo zinaterodi.
30 Mkango, umene ndi wamphamvu kwambiri panyama zonse zakutchire ndiponso umene suopa chilichonse n’kubwerera m’mbuyo,+