2 Mbiri 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Chotero Solomo anasankha amuna 70,000 kuti akhale onyamula katundu, ndi ena 80,000 kuti akhale osema miyala kumapiri.+ Anasankhanso amuna 3,600 kuti akhale owayang’anira.+
2 Chotero Solomo anasankha amuna 70,000 kuti akhale onyamula katundu, ndi ena 80,000 kuti akhale osema miyala kumapiri.+ Anasankhanso amuna 3,600 kuti akhale owayang’anira.+