1 Mafumu 5:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kuwonjezera pa amenewa, panalinso akapitawo a nduna za Solomo+ oyang’anira ntchitoyo. Analipo akapitawo 3,300+ oyang’anira anthu amene anali kugwira ntchitoyo. 1 Mafumu 9:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Palibe ana a Isiraeli amene Solomo anawasandutsa akapolo,+ chifukwa iwo anali ankhondo ake, atumiki ake, akalonga ake, asilikali othandiza pa magaleta, ndiponso atsogoleri a asilikali ake oyendetsa magaleta, ndi a amuna ake okwera pamahatchi.+ 2 Mbiri 2:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Choncho iye anasankhapo amuna 70,000 kuti akhale onyamula katundu,+ amuna 80,000 kuti akhale osema miyala+ kumapiri, ndi amuna 3,600 kuti akhale oyang’anira anthuwo pa ntchito yawo.+
16 Kuwonjezera pa amenewa, panalinso akapitawo a nduna za Solomo+ oyang’anira ntchitoyo. Analipo akapitawo 3,300+ oyang’anira anthu amene anali kugwira ntchitoyo.
22 Palibe ana a Isiraeli amene Solomo anawasandutsa akapolo,+ chifukwa iwo anali ankhondo ake, atumiki ake, akalonga ake, asilikali othandiza pa magaleta, ndiponso atsogoleri a asilikali ake oyendetsa magaleta, ndi a amuna ake okwera pamahatchi.+
18 Choncho iye anasankhapo amuna 70,000 kuti akhale onyamula katundu,+ amuna 80,000 kuti akhale osema miyala+ kumapiri, ndi amuna 3,600 kuti akhale oyang’anira anthuwo pa ntchito yawo.+