2 Mbiri 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mapiko a akerubiwo+ kutalika kwake anali mikono 20. Phiko limodzi linali lalitali mikono isanu kufika kukhoma la chipindacho. Phiko linalo linali lalitali mikono isanu kufika paphiko la kerubi mnzake.+
11 Mapiko a akerubiwo+ kutalika kwake anali mikono 20. Phiko limodzi linali lalitali mikono isanu kufika kukhoma la chipindacho. Phiko linalo linali lalitali mikono isanu kufika paphiko la kerubi mnzake.+