1 Mafumu 6:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Phiko limodzi la kerubi linali lalitali mikono isanu, ndipo phiko linalo linali lalitali mikono isanunso. Kuchokera kunsonga ya phiko lake limodzi kufika kunsonga ya phiko lake lina, kutalika kwake kunali kukwana mikono 10.+
24 Phiko limodzi la kerubi linali lalitali mikono isanu, ndipo phiko linalo linali lalitali mikono isanunso. Kuchokera kunsonga ya phiko lake limodzi kufika kunsonga ya phiko lake lina, kutalika kwake kunali kukwana mikono 10.+