1 Mafumu 6:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Pazitsekopo anajambulapo mochita kugoba akerubi, mitengo ya kanjedza, ndi maluwa ndipo anakuta zojambulazo ndi golide.+
35 Pazitsekopo anajambulapo mochita kugoba akerubi, mitengo ya kanjedza, ndi maluwa ndipo anakuta zojambulazo ndi golide.+