Ezekieli 41:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Pazitseko za kachisi anajambulapo zithunzi za akerubi ndi za mitengo ya kanjedza mochita kugoba.+ Zithunzi zimenezi zinali zofanana ndi zimene anajambula m’makoma. Kutsogolo kwa denga la khonde anakhomako mzere wa matabwa otulukira kunja.
25 Pazitseko za kachisi anajambulapo zithunzi za akerubi ndi za mitengo ya kanjedza mochita kugoba.+ Zithunzi zimenezi zinali zofanana ndi zimene anajambula m’makoma. Kutsogolo kwa denga la khonde anakhomako mzere wa matabwa otulukira kunja.