Ezekieli 41:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ngakhalenso zithunzi zojambula mochita kugoba za akerubi+ ndi za mitengo ya kanjedza,+ zinali ndi miyezo yake. Mitengoyo inali pakati pa kerubi ndi kerubi mnzake, ndipo akerubiwo anali ndi nkhope ziwiriziwiri.+
18 Ngakhalenso zithunzi zojambula mochita kugoba za akerubi+ ndi za mitengo ya kanjedza,+ zinali ndi miyezo yake. Mitengoyo inali pakati pa kerubi ndi kerubi mnzake, ndipo akerubiwo anali ndi nkhope ziwiriziwiri.+