Ezekieli 41:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Pazitseko za kachisi panali zithunzi zojambula mochita kugoba za akerubi ndi za mitengo ya kanjedza zofanana ndi zimene zinali mʼmakoma.+ Kutsogolo kwa denga la khonde anakhomako matabwa otulukira kunja.
25 Pazitseko za kachisi panali zithunzi zojambula mochita kugoba za akerubi ndi za mitengo ya kanjedza zofanana ndi zimene zinali mʼmakoma.+ Kutsogolo kwa denga la khonde anakhomako matabwa otulukira kunja.