-
Ezekieli 41:17, 18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Anayeza pamwamba pa khomo, kunja ndi mkati mwa kachisi komanso kuzungulira khoma lonse la kachisiyo. 18 Kachisiyo anali ndi zithunzi zojambula mochita kugoba za akerubi+ ndi za mitengo ya kanjedza.+ Mtengo uliwonse wa kanjedza unali pakati pa akerubi awiri ndipo kerubi aliyense anali ndi nkhope ziwiri.
-