Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mbiri 3:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Zipilalazo anaziika kumaso kwa kachisi, china mbali ya kudzanja lamanja china mbali ya kumanzere. Chipilala cha mbali ya kudzanja lamanja anachitcha dzina lakuti Yakini, ndipo cha mbali ya kumanzere anachitcha dzina lakuti Boazi.+

  • Chivumbulutso 3:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 “‘Wopambana pa nkhondo, ndidzamuika kukhala mzati+ m’kachisi+ wa Mulungu wanga,+ ndipo sadzachokamonso. Ndidzamulemba dzina la Mulungu wanga, ndiponso dzina la mzinda wa Mulungu wanga, Yerusalemu watsopano,+ wotsika kuchokera kumwamba kwa Mulungu wanga. Ndidzamulembanso dzina langa latsopano.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena