2 Mbiri 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Zipilalazo anaziika kutsogolo kwa kachisi, china anachiika kumanja* china kumanzere.* Chipilala chakumanja anachipatsa dzina lakuti Yakini* ndipo chakumanzere anachipatsa dzina lakuti Boazi.*
17 Zipilalazo anaziika kutsogolo kwa kachisi, china anachiika kumanja* china kumanzere.* Chipilala chakumanja anachipatsa dzina lakuti Yakini* ndipo chakumanzere anachipatsa dzina lakuti Boazi.*