2 Mbiri 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Zipilalazo anaziika kumaso kwa kachisi, china mbali ya kudzanja lamanja china mbali ya kumanzere. Chipilala cha mbali ya kudzanja lamanja anachitcha dzina lakuti Yakini, ndipo cha mbali ya kumanzere anachitcha dzina lakuti Boazi.+
17 Zipilalazo anaziika kumaso kwa kachisi, china mbali ya kudzanja lamanja china mbali ya kumanzere. Chipilala cha mbali ya kudzanja lamanja anachitcha dzina lakuti Yakini, ndipo cha mbali ya kumanzere anachitcha dzina lakuti Boazi.+