2 Mbiri 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kuchindikala kwa thankiyo kunali chikhatho* chimodzi. Mlomo wake unali ngati wa mphika wakukamwa ngati duwa.+ Thankiyo inali yotha kulowa+ madzi okwana mitsuko* 3,000.+
5 Kuchindikala kwa thankiyo kunali chikhatho* chimodzi. Mlomo wake unali ngati wa mphika wakukamwa ngati duwa.+ Thankiyo inali yotha kulowa+ madzi okwana mitsuko* 3,000.+