Miyambo 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 pakuti zimenezi zili ngati nkhata ya maluwa yokongola pamutu pako,+ ndi mkanda wokongola m’khosi mwako.+ Miyambo 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Zidzaika nkhata yamaluwa yokongola kumutu kwako.+ Zidzakuveka chisoti chachifumu chokongola.”+
9 pakuti zimenezi zili ngati nkhata ya maluwa yokongola pamutu pako,+ ndi mkanda wokongola m’khosi mwako.+