3 M’munsi mwa thankiyo munali zokongoletsa zofanana ndi zipanda kuzungulira+ thankiyo, ndipo zinalipo 10 pamkono uliwonse kuzungulira thanki yonseyo.+ Zokongoletsa zooneka ngati zipandazo zinalipo mizere iwiri, ndipo anaziumbira kumodzi ndi thankiyo.