Ekisodo 30:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Upange beseni losambira lamkuwa ndi choikapo chake chamkuwa.+ Uliike pakati pa chihema chokumanako ndi guwa lansembe, ndipo uthiremo madzi.+ Aheberi 9:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 M’malomwake, zimangokhudza zakudya,+ zakumwa,+ ndi miyambo yosiyanasiyana yoviika zinthu m’madzi.+ Zimenezo zinali zofunika za Chilamulo zokhudza zinthu zathupi,+ ndipo zinakhazikitsidwa kufikira nthawi yoikidwiratu yokonzanso zinthu.+
18 “Upange beseni losambira lamkuwa ndi choikapo chake chamkuwa.+ Uliike pakati pa chihema chokumanako ndi guwa lansembe, ndipo uthiremo madzi.+
10 M’malomwake, zimangokhudza zakudya,+ zakumwa,+ ndi miyambo yosiyanasiyana yoviika zinthu m’madzi.+ Zimenezo zinali zofunika za Chilamulo zokhudza zinthu zathupi,+ ndipo zinakhazikitsidwa kufikira nthawi yoikidwiratu yokonzanso zinthu.+