Ekisodo 38:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kenako anapanga beseni losambira lamkuwa+ ndi choikapo chake chamkuwa. Popanga zimenezi anagwiritsa ntchito akalirole* a akazi otumikira, amene anali kutumikira mwadongosolo pachipata cha chihema chokumanako.+ Levitiko 8:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Anawaza ena mwa mafuta odzozerawo maulendo 7 paguwa lansembe+ ndi kudzoza guwa lansembelo, zipangizo zake zonse, beseni ndi choikapo chake, n’kuzipatula. 1 Mafumu 7:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Kenako anapanga mabeseni 10+ amkuwa. Beseni lililonse linali lokwana mitsuko* 40, ndipo linali mikono inayi kukula kwake. Pachotengera chilichonse mwa zotengera 10 zija panali beseni limodzi.
8 Kenako anapanga beseni losambira lamkuwa+ ndi choikapo chake chamkuwa. Popanga zimenezi anagwiritsa ntchito akalirole* a akazi otumikira, amene anali kutumikira mwadongosolo pachipata cha chihema chokumanako.+
11 Anawaza ena mwa mafuta odzozerawo maulendo 7 paguwa lansembe+ ndi kudzoza guwa lansembelo, zipangizo zake zonse, beseni ndi choikapo chake, n’kuzipatula.
38 Kenako anapanga mabeseni 10+ amkuwa. Beseni lililonse linali lokwana mitsuko* 40, ndipo linali mikono inayi kukula kwake. Pachotengera chilichonse mwa zotengera 10 zija panali beseni limodzi.