Ekisodo 30:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Upange beseni losambira lamkuwa ndi choikapo chake chamkuwa.+ Uliike pakati pa chihema chokumanako ndi guwa lansembe, ndipo uthiremo madzi.+ Ekisodo 31:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 guwa lansembe yopsereza ndi zipangizo zake zonse,+ beseni ndi choikapo chake,+ Ekisodo 40:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndipo udzaike beseni pakati pa chihema chokumanako ndi guwa lansembe, ndi kuthiramo madzi.+ Levitiko 8:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Anawaza ena mwa mafuta odzozerawo maulendo 7 paguwa lansembe+ ndi kudzoza guwa lansembelo, zipangizo zake zonse, beseni ndi choikapo chake, n’kuzipatula. 1 Mafumu 7:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Kenako iye anapanga thanki yamkuwa.*+ Pakamwa pa thankiyo panali papakulu mikono 10 kuyeza modutsa pakati pake, ndipo panali pozungulira. Thankiyo inali yaitali mikono isanu kuchokera pansi kufika pamwamba. Pankafunika chingwe chotalika mikono 30 kuti ayeze kuzungulira thankiyo.+
18 “Upange beseni losambira lamkuwa ndi choikapo chake chamkuwa.+ Uliike pakati pa chihema chokumanako ndi guwa lansembe, ndipo uthiremo madzi.+
11 Anawaza ena mwa mafuta odzozerawo maulendo 7 paguwa lansembe+ ndi kudzoza guwa lansembelo, zipangizo zake zonse, beseni ndi choikapo chake, n’kuzipatula.
23 Kenako iye anapanga thanki yamkuwa.*+ Pakamwa pa thankiyo panali papakulu mikono 10 kuyeza modutsa pakati pake, ndipo panali pozungulira. Thankiyo inali yaitali mikono isanu kuchokera pansi kufika pamwamba. Pankafunika chingwe chotalika mikono 30 kuti ayeze kuzungulira thankiyo.+