Ekisodo 38:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Ndiyeno anapanga guwa lansembe zopsereza la matabwa a mthethe, m’litali mwake mikono isanu, ndipo m’lifupi mikono isanu. Guwalo linali lofanana muyezo wake mbali zake zonse zinayi, ndipo msinkhu wake linali mikono itatu.+ Ekisodo 40:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Udzaike guwa lansembe+ zopsereza patsogolo pa khomo la chihema chopatulika, kapena kuti chihema chokumanako.
38 Ndiyeno anapanga guwa lansembe zopsereza la matabwa a mthethe, m’litali mwake mikono isanu, ndipo m’lifupi mikono isanu. Guwalo linali lofanana muyezo wake mbali zake zonse zinayi, ndipo msinkhu wake linali mikono itatu.+
6 “Udzaike guwa lansembe+ zopsereza patsogolo pa khomo la chihema chopatulika, kapena kuti chihema chokumanako.