Ekisodo 27:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 “Upange guwa lansembe la matabwa a mthethe, m’litali mikono isanu, ndipo m’lifupi mikono isanu. Guwalo+ likhale lofanana muyezo wake mbali zake zonse zinayi, ndipo msinkhu wake likhale mikono itatu. Ekisodo 40:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Udzadzozenso guwa lansembe zopsereza ndi ziwiya zake zonse ndi kuliyeretsa.+ Pamenepo guwalo lidzakhala lopatulika kwambiri.+ Aheberi 13:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ife tili ndi guwa lansembe limene ochita utumiki wopatulika kuchihema, alibe ulamuliro wodya za paguwapo.+
27 “Upange guwa lansembe la matabwa a mthethe, m’litali mikono isanu, ndipo m’lifupi mikono isanu. Guwalo+ likhale lofanana muyezo wake mbali zake zonse zinayi, ndipo msinkhu wake likhale mikono itatu.
10 Udzadzozenso guwa lansembe zopsereza ndi ziwiya zake zonse ndi kuliyeretsa.+ Pamenepo guwalo lidzakhala lopatulika kwambiri.+
10 Ife tili ndi guwa lansembe limene ochita utumiki wopatulika kuchihema, alibe ulamuliro wodya za paguwapo.+