27 “Upange guwa lansembe lamatabwa a mthethe,+ mulitali likhale mamita awiri, ndipo mulifupi likhalenso mamita awiri. Guwalo likhale lofanana muyezo wake mbali zake zonse 4, ndipo kutalika kwake kuchokera pansi mpaka mʼmwamba likhale masentimita 134.+