1 Mafumu 7:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Mitu iwiriyo inali pamwamba pa zipilala, komanso inali pamwamba pa mimba imene inagundana ndi maukonde. Kuzungulira mutu uliwonse, panali makangaza 200+ amene anali m’mizere.
20 Mitu iwiriyo inali pamwamba pa zipilala, komanso inali pamwamba pa mimba imene inagundana ndi maukonde. Kuzungulira mutu uliwonse, panali makangaza 200+ amene anali m’mizere.